Ekisodo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo m’mawa mudzaona ulemerero wa Yehova+ chifukwa wamva kung’ung’udza kwanu kotsutsana ndi Yehovayo. Ife ndife ndani kuti muziting’ung’udzira?” Numeri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+ Numeri 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kora atasonkhanitsa khamu+ lonse lotsutsana nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa khamu lonselo.+
7 Ndipo m’mawa mudzaona ulemerero wa Yehova+ chifukwa wamva kung’ung’udza kwanu kotsutsana ndi Yehovayo. Ife ndife ndani kuti muziting’ung’udzira?”
10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+
19 Kora atasonkhanitsa khamu+ lonse lotsutsana nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa khamu lonselo.+