Ekisodo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+ Mateyu 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Musamade nkhawa za tsiku lotsatira,+ chifukwa tsiku lotsatira lidzakhala ndi zodetsa nkhawa zakenso. Zoipa za tsiku lililonse n’zokwanira pa tsikulo.
10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+
34 Musamade nkhawa za tsiku lotsatira,+ chifukwa tsiku lotsatira lidzakhala ndi zodetsa nkhawa zakenso. Zoipa za tsiku lililonse n’zokwanira pa tsikulo.