Ekisodo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Ndikuvumbitsirani mkate kuchokera kumwamba,+ ndipo anthu azipita kukatola. Aliyense azitola muyezo wom’kwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese ngati adzatsatira chilamulo changa kapena ayi.+ Ekisodo 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mose anawauza kuti: “Aliyense asasiyeko chakudyachi mpaka m’mawa.”+
4 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Ndikuvumbitsirani mkate kuchokera kumwamba,+ ndipo anthu azipita kukatola. Aliyense azitola muyezo wom’kwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese ngati adzatsatira chilamulo changa kapena ayi.+