Ekisodo 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero atayandikira msasawo n’kuona mwana wa ng’ombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wa Mose unayaka ndipo nthawi yomweyo anaponya pansi miyala ija ndi kuiswa ali m’tsinde mwa phiri.+ Numeri 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mose atamva zimenezi anakwiya kwambiri, ndipo anauza Yehova kuti: “Nsembe zawo zambewu musaziyang’ane.+ Ine sindinawalande ngakhale bulu mmodzi wamphongo, kapena kuchitira choipa aliyense wa iwo.”+ Aefeso 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwiyani, koma musachimwe.+ Dzuwa lisalowe muli chikwiyire,+
19 Chotero atayandikira msasawo n’kuona mwana wa ng’ombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wa Mose unayaka ndipo nthawi yomweyo anaponya pansi miyala ija ndi kuiswa ali m’tsinde mwa phiri.+
15 Mose atamva zimenezi anakwiya kwambiri, ndipo anauza Yehova kuti: “Nsembe zawo zambewu musaziyang’ane.+ Ine sindinawalande ngakhale bulu mmodzi wamphongo, kapena kuchitira choipa aliyense wa iwo.”+