Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ine ndaima pamaso panu. Munditsutse pamaso pa Yehova ndi pamaso pa wodzozedwa+ wake: Alipo kodi amene ndinam’tengerapo ng’ombe kapena bulu wake?+ Alipo kodi amene ndinam’chitirapo chinyengo, kapena kum’pondereza? Kodi ndinalandirapo chiphuphu kwa aliyense kuti ndisaone zimene anachita?+ Ndili wokonzeka kukubwezerani anthu inu.”+

  • Machitidwe 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Sindinasirire mwa nsanje siliva, golide kapena chovala cha munthu.+

  • 2 Akorinto 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tipatseni malo m’mitima mwanu.+ Ifetu sitinalakwire aliyense, sitinaipitse aliyense, ndipo sitinachenjerere aliyense.+

  • 1 Petulo 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena