Ekisodo 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ananyamuka ku Refidimu+ n’kulowa m’chipululu cha Sinai+ ndi kumanga msasa wawo m’chipululumo. Aisiraeli anamanga msasawo pafupi ndi phiri la Sinai.+ 1 Mafumu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anatha kuyenda masiku 40,+ usana ndi usiku, mpaka kukafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+
2 Ananyamuka ku Refidimu+ n’kulowa m’chipululu cha Sinai+ ndi kumanga msasa wawo m’chipululumo. Aisiraeli anamanga msasawo pafupi ndi phiri la Sinai.+
8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anatha kuyenda masiku 40,+ usana ndi usiku, mpaka kukafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+