Yeremiya 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+ Mateyu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba. Mateyu 24:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Koma dziwani ichi: Ngati mwininyumba angadziwe nthawi yobwera mbala,+ angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.
26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+
20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba.
43 “Koma dziwani ichi: Ngati mwininyumba angadziwe nthawi yobwera mbala,+ angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.