Levitiko 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kapena watola chinthu chotayika+ koma akukana kuti sanachitole, ndipo walumbira monama+ pa chilichonse chimene munthu angachite n’kuchimwa nacho, Miyambo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+
3 kapena watola chinthu chotayika+ koma akukana kuti sanachitole, ndipo walumbira monama+ pa chilichonse chimene munthu angachite n’kuchimwa nacho,
9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+