Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 iye alumbire+ kwa mnzake pamaso pa Yehova kuti si iye amene wachita zimenezo pa katundu wa mnzake.+ Mwini wa katunduyo azivomereza lumbirolo ndipo mnzakeyo asalipire.

  • Levitiko 19:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Musamalumbire zabodza m’dzina langa+ ndi kuipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova.

  • Yeremiya 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+

  • Malaki 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Anthu inu ndidzakuyandikirani kuti ndikuweruzeni.+ Sindidzazengereza kupereka umboni+ wotsutsa amatsenga,+ achigololo,+ olumbira monama+ komanso ochita chinyengo pa malipiro a munthu waganyu.+ Sindidzazengereza kupereka umboni wotsutsa anthu ochitira chinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye*+ ndiponso opondereza alendo.+ Anthu amenewa sakundiopa,”+ watero Yehova wa makamu.

  • Aefeso 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+

  • Akolose 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Musamanamizane.+ Vulani umunthu+ wakale pamodzi ndi ntchito zake,

  • 1 Timoteyo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena