Ekisodo 21:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 mwiniwake wa dzenjelo azilipira.+ Malipirowo azipereka kwa mwiniwake wa ng’ombeyo, koma iye azitenga nyama yakufayo. Levitiko 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu amene wakantha ndi kupha chiweto cha mnzake, azibweza chiweto china, chiweto kulipira chiweto.+
34 mwiniwake wa dzenjelo azilipira.+ Malipirowo azipereka kwa mwiniwake wa ng’ombeyo, koma iye azitenga nyama yakufayo.
18 Munthu amene wakantha ndi kupha chiweto cha mnzake, azibweza chiweto china, chiweto kulipira chiweto.+