Ekisodo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Moto ukabuka n’kugwirira zomera zaminga, ndipo wafalikira m’munda n’kutentha mitolo yambewu, mbewu zosadula kapena munda wonse,+ amene anayatsa motowo azilipira ndithu chifukwa cha zotenthedwazo. Ekisodo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Koma ngati munthu wabwereka chiweto kwa mnzake+ ndipo chalumala kapena chafa mwiniwake palibe, wobwerekayo azilipira ndithu.+ Deuteronomo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ukamanga nyumba yatsopano uzimanganso kampanda padenga*+ la nyumbayo kuopera kuti ungaike mlandu wa magazi panyumba yako ngati munthu atagwa kuchokera padengapo.
6 “Moto ukabuka n’kugwirira zomera zaminga, ndipo wafalikira m’munda n’kutentha mitolo yambewu, mbewu zosadula kapena munda wonse,+ amene anayatsa motowo azilipira ndithu chifukwa cha zotenthedwazo.
14 “Koma ngati munthu wabwereka chiweto kwa mnzake+ ndipo chalumala kapena chafa mwiniwake palibe, wobwerekayo azilipira ndithu.+
8 “Ukamanga nyumba yatsopano uzimanganso kampanda padenga*+ la nyumbayo kuopera kuti ungaike mlandu wa magazi panyumba yako ngati munthu atagwa kuchokera padengapo.