Levitiko 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Usagone ndi nyama iliyonse*+ n’kukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kumeneko n’kuchita zosemphana ndi chibadwa. Levitiko 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Mwamuna akagona ndi nyama,*+ aziphedwa ndithu ndipo muziphanso nyamayo. Deuteronomo 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona nyama iliyonse.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
23 “‘Usagone ndi nyama iliyonse*+ n’kukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kumeneko n’kuchita zosemphana ndi chibadwa.
21 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona nyama iliyonse.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)