Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zitatero, Isaki anayamba kubzala mbewu m’dzikomo.+ M’chaka chimenechi anakolola zochuluka moti pa mbewu zimene anabzala, anakolola zochuluka kuwirikiza nthawi 100,+ popeza Yehova anali kum’dalitsa.+

  • Deuteronomo 28:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova adzaika madalitso pankhokwe+ ndi pa zochita zako zonse+ ndipo adzakudalitsa m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.

  • Malaki 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Bweretsani gawo limodzi mwa magawo 10 alionse a zinthu zanu+ n’kuziika mosungiramo zinthu zanga, kuti m’nyumba mwanga mukhale chakudya.+ Ndiyeseni chonde pa nkhani imeneyi,+ kuti muone ngati sindidzakutsegulirani zipata za kumwamba+ ndi kukukhuthulirani madalitso oti mudzasowa powalandirira,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena