Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ 1 Mafumu 8:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 (popeza iwo ndi anthu anu ndi cholowa chanu,+ amene munawatulutsa ku Iguputo,+ kuwachotsa m’ng’anjo yachitsulo).+
51 (popeza iwo ndi anthu anu ndi cholowa chanu,+ amene munawatulutsa ku Iguputo,+ kuwachotsa m’ng’anjo yachitsulo).+