Levitiko 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo wansembe azitentha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi. Mafuta onse ndi a Yehova.+ Levitiko 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Koma mafuta onse a ng’ombe ya nsembe yamachimo, aziwachotsa. Azichotsa mafuta okuta matumbo, mafuta onse okuta matumbo.+
16 Ndipo wansembe azitentha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi. Mafuta onse ndi a Yehova.+
8 “‘Koma mafuta onse a ng’ombe ya nsembe yamachimo, aziwachotsa. Azichotsa mafuta okuta matumbo, mafuta onse okuta matumbo.+