Levitiko 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Aroni anapha nyama ya nsembe yopsereza, ndipo ana ake anam’patsa magazi a nyamayo. Pamenepo iye anawaza magaziwo mozungulira paguwa lansembe.+ 2 Mbiri 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo anapha+ ng’ombezo ndipo ansembe anatenga magazi+ ake n’kuwaza+ paguwa lansembe. Kenako anapha nkhosa zamphongo+ zija n’kuwaza magazi ake paguwa lansembe. Atatero anapha ana a nkhosa amphongo aja n’kuwaza magazi+ ake paguwa lansembe.
12 Ndiyeno Aroni anapha nyama ya nsembe yopsereza, ndipo ana ake anam’patsa magazi a nyamayo. Pamenepo iye anawaza magaziwo mozungulira paguwa lansembe.+
22 Iwo anapha+ ng’ombezo ndipo ansembe anatenga magazi+ ake n’kuwaza+ paguwa lansembe. Kenako anapha nkhosa zamphongo+ zija n’kuwaza magazi ake paguwa lansembe. Atatero anapha ana a nkhosa amphongo aja n’kuwaza magazi+ ake paguwa lansembe.