Levitiko 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Lamulo la nsembe ya kupalamula+ lili motere: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+