Levitiko 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako azidontheza ena mwa magazi a nsembe yamachimo m’mbali mwa guwa lansembe, koma magazi otsalawo aziwathira pansi pa guwa lansembelo.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo. Aheberi 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+
9 Kenako azidontheza ena mwa magazi a nsembe yamachimo m’mbali mwa guwa lansembe, koma magazi otsalawo aziwathira pansi pa guwa lansembelo.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.
22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+