Levitiko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyama ya nsembe ya kupalamula aziiphera pamalo+ amene nthawi zonse amaphera nyama ya nsembe yopsereza, ndipo magazi ake+ aziwazidwa+ mozungulira paguwa lansembe. Aheberi 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+
5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.
2 Nyama ya nsembe ya kupalamula aziiphera pamalo+ amene nthawi zonse amaphera nyama ya nsembe yopsereza, ndipo magazi ake+ aziwazidwa+ mozungulira paguwa lansembe.
22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+