Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Ngati mukupereka nsembe yambewu yophikidwa mu uvuni, izikhala ya ufa wabwino kwambiri. Muzipereka mkate wozungulira woboola pakati,+ wopanda chofufumitsa, wothira mafuta, kapena timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa,+ topaka mafuta.+

  • Levitiko 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda chofufumitsa+ ndi kudya mkatewo m’malo oyera. Aziudyera m’bwalo la chihema chokumanako.

  • Numeri 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Aperekenso dengu la mikate yozungulira yoboola pakati. Mikateyo ikhale yopanda chofufumitsa, yophika ndi ufa wosalala,+ ndi yopaka mafuta.+ M’dengumo mukhalenso timikate topyapyala topanda chofufumitsa topaka mafuta,+ limodzi ndi nsembe yake yambewu,+ ndiponso nsembe zake zachakumwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena