Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 mkate wopanda chofufumitsa, mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta ndi timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta.+ Uzipange ndi ufa wa tirigu wosalala.

  • Levitiko 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma nsembe yambewu iliyonse yothira mafuta+ kapena youma+ izikhala ya ana onse aamuna a Aroni, azigawana mofanana.

  • Numeri 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Aperekenso dengu la mikate yozungulira yoboola pakati. Mikateyo ikhale yopanda chofufumitsa, yophika ndi ufa wosalala,+ ndi yopaka mafuta.+ M’dengumo mukhalenso timikate topyapyala topanda chofufumitsa topaka mafuta,+ limodzi ndi nsembe yake yambewu,+ ndiponso nsembe zake zachakumwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena