Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+ 1 Akorinto 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taganizirani zochitika za Isiraeli wakuthupi:+ Kodi amene amadyako zoperekedwa nsembe sindiye kuti akugawana ndi guwa lansembe?+
3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+
18 Taganizirani zochitika za Isiraeli wakuthupi:+ Kodi amene amadyako zoperekedwa nsembe sindiye kuti akugawana ndi guwa lansembe?+