Ekisodo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anatuma anyamata a Isiraeli ndipo anyamatawo anapereka nsembe zopsereza komanso anapereka ng’ombe kuti zikhale nsembe zachiyanjano+ kwa Yehova. Levitiko 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli+ kuti, ‘Munthu aliyense akafuna kupereka chiweto kwa Yehova kuti ikhale nsembe, azipereka ng’ombe, nkhosa kapena mbuzi.
5 Kenako anatuma anyamata a Isiraeli ndipo anyamatawo anapereka nsembe zopsereza komanso anapereka ng’ombe kuti zikhale nsembe zachiyanjano+ kwa Yehova.
2 “Uza ana a Isiraeli+ kuti, ‘Munthu aliyense akafuna kupereka chiweto kwa Yehova kuti ikhale nsembe, azipereka ng’ombe, nkhosa kapena mbuzi.