Genesis 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Nowa anamangira Yehova guwa lansembe.+ Atatero, anatenga zina mwa nyama zonse zoyera,+ ndi zina mwa zouluka zonse zoyera,+ n’kuzipereka nsembe yopsereza paguwapo.+ Ekisodo 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhosa yonseyo uitenthe paguwa lansembe. Imeneyo ndi nsembe yopsereza+ yoperekedwa kwa Yehova, fungo lokhazika mtima pansi.+ Ndiyo nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
20 Tsopano Nowa anamangira Yehova guwa lansembe.+ Atatero, anatenga zina mwa nyama zonse zoyera,+ ndi zina mwa zouluka zonse zoyera,+ n’kuzipereka nsembe yopsereza paguwapo.+
18 Nkhosa yonseyo uitenthe paguwa lansembe. Imeneyo ndi nsembe yopsereza+ yoperekedwa kwa Yehova, fungo lokhazika mtima pansi.+ Ndiyo nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.