Ekisodo 28:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+
40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+