Ekisodo 39:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anawomba mikanjo ya Aroni ndi ana ake ya ulusi wabwino kwambiri.+ Levitiko 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni+ ndi kuwaveka mikanjo, kuwamanga malamba a pamimba,+ ndi kuwakulunga mipango+ kumutu, monga mmene Yehova analamulira Mose. 1 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Samueli anali kutumikira+ pamaso pa Yehova, ali mwana ndipo anali kuvala efodi wansalu.+
13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni+ ndi kuwaveka mikanjo, kuwamanga malamba a pamimba,+ ndi kuwakulunga mipango+ kumutu, monga mmene Yehova analamulira Mose.