Levitiko 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mose anati: “Mverani zimene Yehova walamula kuti muchite, kuti ulemerero wa Yehova uonekere kwa inu.”+ Numeri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+ Numeri 16:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Khamulo litasonkhana pamodzi kuti liukire Mose ndi Aroni, linacheukira kuchihema chokumanako. Anthuwo anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho, ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+
6 Ndiyeno Mose anati: “Mverani zimene Yehova walamula kuti muchite, kuti ulemerero wa Yehova uonekere kwa inu.”+
10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+
42 Khamulo litasonkhana pamodzi kuti liukire Mose ndi Aroni, linacheukira kuchihema chokumanako. Anthuwo anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho, ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+