Ekisodo 28:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndipo uveke Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwapatse mphamvu*+ ndi kuwayeretsa, ndipo atumikire monga ansembe anga. Levitiko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+
41 Ndipo uveke Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwapatse mphamvu*+ ndi kuwayeretsa, ndipo atumikire monga ansembe anga.
12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+