Ekisodo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kenako upereke ng’ombe patsogolo pa chihema chokumanako, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa ng’ombeyo.+ Levitiko 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anatenga nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu pa nkhosayo.+
10 “Kenako upereke ng’ombe patsogolo pa chihema chokumanako, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa ng’ombeyo.+
18 Kenako anatenga nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu pa nkhosayo.+