Ekisodo 12:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Lamulo lililonse ligwire ntchito mofanana kwa mbadwa ndi kwa mlendo wokhala pakati panu.”+ Deuteronomo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inunso muzikonda mlendo wokhala pakati panu,+ chifukwa munali alendo m’dziko la Iguputo.+