Deuteronomo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inunso muzikonda mlendo, chifukwa nanunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+