Deuteronomo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inunso muzikonda mlendo wokhala pakati panu,+ chifukwa munali alendo m’dziko la Iguputo.+