Levitiko 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa. Muzim’konda mmene mumadzikondera nokha,+ chifukwa inunso munali alendo m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa. Muzim’konda mmene mumadzikondera nokha,+ chifukwa inunso munali alendo m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.