Levitiko 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Usavule mkazi wa bambo ako,+ chifukwa kumeneko n’kuvula bambo ako. Deuteronomo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wavula bambo akewo.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
20 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wavula bambo akewo.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)