Levitiko 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Usagone ndi nyama iliyonse*+ n’kukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kumeneko n’kuchita zosemphana ndi chibadwa.
23 “‘Usagone ndi nyama iliyonse*+ n’kukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kumeneko n’kuchita zosemphana ndi chibadwa.