Levitiko 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nyama imene mavalo+ ake anawafinya, kuwatswanya, kuwathothola kapena kuwadula, musaipereke kwa Yehova, ngakhalenso m’dziko lanu musadzapereke nsembe nyama zoterezi. Deuteronomo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Mwamuna wofulidwa+ mwa kuphwanya mavalo+ ake kapena woduka maliseche asalowe mumpingo wa Yehova.
24 Nyama imene mavalo+ ake anawafinya, kuwatswanya, kuwathothola kapena kuwadula, musaipereke kwa Yehova, ngakhalenso m’dziko lanu musadzapereke nsembe nyama zoterezi.