Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Chotero kachitsuloko kazikhala pamphumi pa Aroni, ndipo Aroni aziyankha mlandu wa machimo ochimwira zinthu zopatulika,+ zimene ana a Isiraeli adzaziyeretsa. Izi ndizo mphatso zawo zonse zopatulika. Kachitsuloko kazikhala pamphumi pake nthawi zonse, kuti azichititsa anthuwo kukhala ovomerezeka+ pamaso pa Yehova.

  • Numeri 18:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Musachimwe polephera kupereka gawo labwino koposa la zinthuzo, ndipo musaipitse zinthu zopatulika za ana a Isiraeli, kuti mungafe.’”+

  • Deuteronomo 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ng’ombe kapena wa nkhosa uzim’patulira Yehova Mulungu wako.+ Usagwiritse ntchito mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe, kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena