Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno munthu wosadetsedwa+ atenge kamtengo ka hisope.+ Akaviike m’madziwo n’kuwaza hemalo. Awazenso ziwiya zonse ndi anthu onse amene anali muhemalo. Komanso, awaze munthu amene anakhudza fupa la munthu, kapena kukhudza munthu wophedwa, kapenanso mtembo uliwonse, ngakhalenso manda a munthu.

  • Aheberi 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 M’malomwake, zimangokhudza zakudya,+ zakumwa,+ ndi miyambo yosiyanasiyana yoviika zinthu m’madzi.+ Zimenezo zinali zofunika za Chilamulo zokhudza zinthu zathupi,+ ndipo zinakhazikitsidwa kufikira nthawi yoikidwiratu yokonzanso zinthu.+

  • Aheberi 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti ngati magazi a mbuzi+ ndi a ng’ombe zamphongo+ komanso phulusa+ la ng’ombe yaikazi imene sinaberekepo, zimene amawaza nazo anthu oipitsidwa,+ zimawayeretsa mpaka kukhaladi oyera pamaso pa Mulungu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena