Numeri 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuchokera ku fuko la Benjamini,+ Abidana+ mwana wa Gidoni, Numeri 7:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Pa tsiku la 9 panali mtsogoleri+ wa ana a Benjamini, Abidana+ mwana wa Gidoni. Numeri 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Benjamini+ anali Abidana,+ mwana wa Gidoni.