Numeri 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Benjamini.+ Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidoni. Numeri 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Benjamini+ anali Abidana,+ mwana wa Gidoni.
22 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Benjamini.+ Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidoni.