Numeri 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kuchokera ku fuko la Aseri,+ Pagiyeli+ mwana wa Okirani, Numeri 7:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Pa tsiku la 11 panali mtsogoleri wa ana a Aseri, Pagiyeli+ mwana wa Okirani. Numeri 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Aseri+ anali Pagiyeli,+ mwana wa Okirani.