Genesis 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanditcha wodala.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Aseri.*+ Genesis 49:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Chakudya chochokera kwa Aseri chidzakhala chonona,+ ndipo chakudya chokoma cha mfumu chidzachokera kwa iye.+
13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanditcha wodala.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Aseri.*+
20 “Chakudya chochokera kwa Aseri chidzakhala chonona,+ ndipo chakudya chokoma cha mfumu chidzachokera kwa iye.+