Deuteronomo 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kwa Aseri anati:+“Aseri ndi wodalitsidwa ndi ana aamuna.+Akhale wovomerezeka ndi abale ake,+Woponda phazi lake m’mafuta.+ Yoswa 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Maere achisanu+ anagwera fuko la ana a Aseri,+ potsata mabanja awo. 1 Mafumu 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anali ndi nduna 12 mu Isiraeli yense, zomwe zinkabweretsa chakudya kwa mfumu ndi banja lake lachifumu. Nduna iliyonse inali ndi udindo wobweretsa chakudya kwa mwezi umodzi pachaka.+ 1 Mafumu 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Baana mwana wa Husai, ku Aseri+ ndi ku Bealoti,
24 Kwa Aseri anati:+“Aseri ndi wodalitsidwa ndi ana aamuna.+Akhale wovomerezeka ndi abale ake,+Woponda phazi lake m’mafuta.+
7 Solomo anali ndi nduna 12 mu Isiraeli yense, zomwe zinkabweretsa chakudya kwa mfumu ndi banja lake lachifumu. Nduna iliyonse inali ndi udindo wobweretsa chakudya kwa mwezi umodzi pachaka.+