Numeri 26:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Njira yokha imene ugawire dzikolo ndiyo mwa kuchita maere basi.+ Onse alandire cholowacho potsata mayina a mafuko a makolo awo. Yoswa 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma anthu inu, mukagawe dzikolo m’zigawo 7 ndipo mukazilembe. Mukakatero, mukabwere nazo kuno kwa ine kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.
55 Njira yokha imene ugawire dzikolo ndiyo mwa kuchita maere basi.+ Onse alandire cholowacho potsata mayina a mafuko a makolo awo.
6 Koma anthu inu, mukagawe dzikolo m’zigawo 7 ndipo mukazilembe. Mukakatero, mukabwere nazo kuno kwa ine kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.