-
Luka 2:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Kunalinso Anna mneneri wamkazi, mwana wa Fanueli, wa fuko la Aseri. Mayi ameneyu anali wachikulire kwambiri, ndipo anakhala ndi mwamuna wake zaka 7 zokha kuchokera pa unamwali wake.
-