Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ana amene Zilipa kapolo wa Leya anaberekera Yakobo anali Gadi ndi Aseri. Amenewa ndiwo ana aamuna a Yakobo amene anabereka ku Padana-ramu.

  • Genesis 46:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ana a Aseri+ anali Imuna, Isiva, Isivi ndi Beriya.+ Panalinso mlongo wawo Sera.

      Ana a Beriya anali Hiberi ndi Malikieli.+

  • Genesis 49:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Chakudya chochokera kwa Aseri chidzakhala chonona,+ ndipo chakudya chokoma cha mfumu chidzachokera kwa iye.+

  • Deuteronomo 33:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kwa Aseri anati:+

      “Aseri ndi wodalitsidwa ndi ana aamuna.+

      Akhale wovomerezeka ndi abale ake,+

      Woponda phazi lake m’mafuta.+

  • Chivumbulutso 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mu fuko la Aseri,+ 12,000.

      Mu fuko la Nafitali,+ 12,000.

      Mu fuko la Manase,+ 12,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena