Ekisodo 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho iwo anafunsa Mose kuti: “Kodi watibweretsa kuno kuti tidzafere m’chipululu muno chifukwa chakuti mu Iguputo mulibe manda?+ N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi, kutitulutsa mu Iguputo? Ekisodo 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo anthu anayamba kung’ung’udza motsutsana ndi Mose,+ kuti: “Timwa chiyani?” Numeri 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi ukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti unatichotsa kudziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere m’chipululu muno,+ kutinso ukhale ngati mfumu yomatilamula?+
11 Choncho iwo anafunsa Mose kuti: “Kodi watibweretsa kuno kuti tidzafere m’chipululu muno chifukwa chakuti mu Iguputo mulibe manda?+ N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi, kutitulutsa mu Iguputo?
13 Kodi ukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti unatichotsa kudziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere m’chipululu muno,+ kutinso ukhale ngati mfumu yomatilamula?+