Ekisodo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo ana a Isiraeli anali kunena kwa Mose ndi Aroni kuti: “Zikanakhala bwino dzanja la Yehova likanatiphera+ m’dziko la Iguputo, kumene tinali kudya nyama+ ndipo tinali kudya mkate ndi kukhuta. M’malomwake mwatibweretsa m’chipululu muno kuti muphetse mpingo wonsewu ndi njala.”+ Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+
3 Ndipo ana a Isiraeli anali kunena kwa Mose ndi Aroni kuti: “Zikanakhala bwino dzanja la Yehova likanatiphera+ m’dziko la Iguputo, kumene tinali kudya nyama+ ndipo tinali kudya mkate ndi kukhuta. M’malomwake mwatibweretsa m’chipululu muno kuti muphetse mpingo wonsewu ndi njala.”+
29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+