Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho anthu anamva ludzu pamenepo, ndipo anthuwo anapitiriza kung’ung’udzira Mose kuti: “N’chifukwa chiyani unatitulutsa mu Iguputo kuti udzatiphe ndi ludzu, ifeyo pamodzi ndi ana athu ndi ziweto zathu?”+

  • Numeri 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kodi ukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti unatichotsa kudziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere m’chipululu muno,+ kutinso ukhale ngati mfumu yomatilamula?+

  • Deuteronomo 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anakuphunzitsani kudzichepetsa pokukhalitsani ndi njala+ ndi kukudyetsani mana,+ amene inu kapena makolo anu sanawadziwe. Anachita zimenezi kuti mudziwe kuti munthu sakhala ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse ochokera m’kamwa mwa Yehova.+

  • Maliro 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Amene anaphedwa ndi lupanga+ aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala,+

      Pakuti amene anafa ndi njala anafooka chifukwa chosowa chakudya, ndipo anakhala ngati apyozedwa ndi lupanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena