Numeri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chiyani munatitulutsa m’dziko la Iguputo kutibweretsa kumalo oipa ano?+ Malo anji osamera mbewu iliyonse? Mitengo ya nkhuyu kulibe kuno, ngakhale mitengo ya mpesa, kapena mitengo ya makangaza.+ Ndi madzi akumwa omwe kulibe!”
5 N’chifukwa chiyani munatitulutsa m’dziko la Iguputo kutibweretsa kumalo oipa ano?+ Malo anji osamera mbewu iliyonse? Mitengo ya nkhuyu kulibe kuno, ngakhale mitengo ya mpesa, kapena mitengo ya makangaza.+ Ndi madzi akumwa omwe kulibe!”